book.jayu.org

Kodi mwabadwadi mwatsopano mwa madzi ndi mzimu woyera?

Paul C. Jong, [zithunzi: Young-ae Kim], [womasulira: Samson Lungu, Ezekiel, Ruth, Abigail]

bHephzibah Publishing House·2024-11-01

  • 417쪽
  • 148×210mm
  • 종교

로그인하면 내 서재에 추가할 수 있어요.

책 소개

Mutu waukulu wa bukuli ndi "kubadwa mwatsopano mwa Madzi ndi Mzimu Woyera." Ili ndi chiyambi chake pa mutuwu. Mwanjira ina, bukuli limatiwuza momveka bwino chomwe kubadwa mwatsopano kuli ndi mmene tingabadwire mwatsopano mwa madzi ndi Mzimu Woyera molingana ndi Baibulo. Madzi amaimira ubatizo wa Yesu ku Yordano ndipo Baibulo limati machimo athu onse anaperekedwa kwa Yesu pamene Iye anabatizidwa ndi Yohane Mbatizi. Yohane anali woimira anthu onse ndiponso mdzukulu wa Aroni, Wansembe Wamkulu. Aroni anasanjika manja ake pamutu pa mbuzi yopereka nsembe ndipo anapititsira machimo onse a chaka cha Aisraeli pa iyo pa Tsiku la Chiyanjanitso. Ichi ndi chithunzithunzi cha zinthu zabwino zikubwera. Ubatizo wa Yesu ndi chifaniziro cha kusanjika manja. Yesu anabatizidwa m`njira ya kusanjika manja ku Yordano. Choncho Iye anachotsa machimo onse a dziko lapansi kudzera mu ubatizo Wake ndipo anapachikidwa kuti alipire machimowo. Koma Akhristu ambiri sadziwa chifukwa chake Yesu anabatizidwa ndi Yohane Mbatizi mu Yordano. Ubatizo wa Yesu ndi mawu ofunika kwambiri a bukuli ndiponso gawo losatheka kuchotsa la Uthenga Wabwino wa Madzi ndi Mzimu Woyera. Tikhoza kubadwa mwatsopano pokhapokha titakhulupirira mu ubatizo wa Yesu ndi Mtanda Wake.

목차펼치기

ZAM’KATIMU Chigawo Choyamba — Maulaliki 1. Choyamba Ife Tiyenera Kudziwa Machimo Athu kuti Tiomboledwe (Marko 7:8-9, 20-23) ------------------ 21 2. Anthu Amabadwa Wochimwa (Marko 7:20-23) ---------------------------------------------- 41 3. Ngati Ife Tichita Zinthu Motsatira Lamulo, Kodi Ilo Lingatipulutse Ife? (Luka 10:25-30) ------------- 55 4. Chiombolo cha Muyaya (Yohane 8:1-12) -------------------- 79 5. Ubatizo wa Yesu ndi Chitetezero cha Machimo (Mateyu 3:13-17) ------------------------------------------- 115 6. Yesu Kristu Adadza mwa Madzi, Mwazi, ndi Mzimu Woyera (1 Yohane 5:1-12) ----------------------- 171 7. Ubatizo wa Yesu Ndi Chifaniziro cha Chipulumutso cha Ochimwa (1 Petro 3:20-22) --------------------------- 211 8. Uthenga Wabwino wa Chiombolo Chochuluka (Yohane 13:1-17) ------------------------------------------- 233 Chigawo Chachiwiri — Mau Owonjezera 1. Umboni wa Chipulumutso ------------------------------------ 307 2. Kufotokoza Kowonjezera ------------------------------------- 329 3. Mafunso ndi Mayankho --------------------------------------- 367

출처: 국립중앙도서관 서지정보

리뷰 남기기

로그인하면 리뷰를 남길 수 있어요.

리뷰 0개

아직 리뷰가 없어요.